2 Samueli 23:35 - Buku Lopatulika Heziro wa ku Karimele, Paarai Mwaraba; Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Heziro wa ku Karimele, Paarai Mwaraba; Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Heziro wa ku Karimele, Paarai Mwaraba, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Heziro wa ku Karimeli, Paarai Mwaribi, |
Ndipo Samuele analawirira m'mawa kuti akakomane ndi Saulo; ndipo munthu anamuuza Samuele kuti, Saulo anafika ku Karimele, ndipo taonani, anaimika chikumbutso chake, nazungulira, napitirira, natsikira ku Giligala.