Ndipo kunali chitapita ichi, kunalinso nkhondo ndi Afilisti ku Gobu; pamenepo Sibekai Muhusa anapha Safi, ndiye wa ana a Rafa.
2 Samueli 23:27 - Buku Lopatulika Abiyezere Mwanatoti, Mebunai Muhusa; Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Abiyezere Mwanatoti, Mebunai Muhusa; Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Abiyezere wa ku Anatoti, Mebunai Muhusa, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Abiezeri wa ku Anatoti, Sibekai Mhusati, |
Ndipo kunali chitapita ichi, kunalinso nkhondo ndi Afilisti ku Gobu; pamenepo Sibekai Muhusa anapha Safi, ndiye wa ana a Rafa.
nati, Pali Mulungu wanga, kukhale kutali kwa ine kuchita ichi. Ngati ndidzamwa mwazi wa anthu awa? Akadataya moyo wao, inde akadataya moyo wao, pakukatenga madziwa. M'mwemo sanafune kuwamwa. Izi anazichita atatu amphamvuwa.
Wachisanu ndi chinai wa mwezi wachisanu ndi chinai ndiye Abiyezere Mwanatoti wa Abenjamini; ndi m'chigawo mwake zikwi makumi awiri mphambu zinai.