Ndipo Yowabu mwana wa Zeruya anayang'anira ankhondo, ndi Yehosafati mwana wa Ahiludi anali wolemba mbiri,
2 Samueli 20:24 - Buku Lopatulika ndi Adoramu anayang'anira msonkho; ndi Yehosafati mwana wa Ahiludi anali wolemba mbiri; Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 ndi Adoramu anayang'anira msonkho; ndi Yehosafati mwana wa Ahiludi anali wolemba mbiri; Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Adoniramu anali mkulu woyang'anira za thangata. Yehosafati, mwana wa Ahiludi, anali mlembi wolemba mbiri ya dziko. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Adoramu amayangʼanira anthu ogwira ntchito ya thangata, Yehosafati mwana wa Ahiludi anali mlembi wa zochitika, |
Ndipo Yowabu mwana wa Zeruya anayang'anira ankhondo, ndi Yehosafati mwana wa Ahiludi anali wolemba mbiri,
Pamenepo mfumu Rehobowamu anatuma Adoramu wamsonkho, ndipo Aisraele onse anamponya miyala, nafa. Ndipo mfumu Rehobowamu anafulumira kulowa m'galeta wake kuthawira ku Yerusalemu.
ndi Ahisara anayang'anira banja la mfumu, ndi Adoniramu mwana wa Abida anali wamsonkho.