Pomwepo Abisalomu anati, Kaitane tsopano Husai Mwariki yemwe, timvenso chimene anene iye.
2 Samueli 15:37 - Buku Lopatulika Chomwecho Husai bwenzi la Davide anadza m'mzindamo; ndipo Abisalomu anafika ku Yerusalemu. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Chomwecho Husai bwenzi la Davide anadza m'mudzimo; ndipo Abisalomu anafika ku Yerusalemu. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Choncho Husai, bwenzi la Davide, adaloŵa mu mzinda, nthaŵi yomwe Abisalomu ankaloŵa mu Yerusalemu. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ndipo Husai bwenzi la Davide anafika ku Yerusalemu pamene Abisalomu amalowa mu mzinda. |
Pomwepo Abisalomu anati, Kaitane tsopano Husai Mwariki yemwe, timvenso chimene anene iye.
ndi Azariya mwana wa Natani anayang'anira akapitao, ndipo Zabudi mwana wa Natani anali wansembe ndi nduna yopangira mfumu,