Baibulo la pa intaneti

Zotsatsa


Baibulo lonse Chipangano Chakale Chipangano Chatsopano




2 Samueli 15:33 - Buku Lopatulika

Ndipo Davide ananena naye, Ukapita pamodzi ndi ine udzandilemetsa;

Onani mutuwo

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

Ndipo Davide ananena naye, Ukapita pamodzi ndi ine udzandilemetsa;

Onani mutuwo

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

Davide adamuuza kuti, “Ukapita nane, sizindithandiza kwenikweni.

Onani mutuwo

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

Davide anati kwa iye, “Ngati iwe upite ndi ine, udzakhala chondilemetsa.

Onani mutuwo



2 Samueli 15:33
2 Mawu Ofanana  

koma ukabwerera kumzinda, ndi kunena ndi Abisalomu, Ine ndine mnyamata wanu, mfumu; monga kale ndinali mnyamata wa atate wanu, momwemo tsopano ndidzakhala mnyamata wanu; pomwepo udzanditsutsira uphungu wa Ahitofele.


Lero ndili nazo zaka makumi asanu ndi atatu; kodi ndikhoza kuzindikiranso kusiyanitsa zabwino ndi zoipa? Mnyamata wanu ndikhoza kodi kuzindikira chimene ndidya kapena kumwa? Kodi ndikhozanso kumva mau a amuna ndi akazi oimba? Chifukwa ninji tsono mnyamata wanu ndidzakhalanso wolemetsa mbuye wanga mfumu.