Ndipo mfumu Solomoni anapereka nsembe ya ng'ombe zikwi makumi awiri mphambu ziwiri, ndi nkhosa zikwi makumi awiri. Momwemo mfumu ndi anthu onse anapereka nyumba ya Mulungu.
2 Mbiri 7:4 - Buku Lopatulika Pamenepo mfumu ndi anthu onse anapereka nsembe pamaso pa Yehova. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Pamenepo mfumu ndi anthu onse anapereka nsembe pamaso pa Yehova. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Tsono mfumu pamodzi ndi anthu onsewo adapereka nsembe pamaso pa Chauta. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Tsono mfumu ndi anthu onse anapereka nsembe pamaso pa Yehova. |
Ndipo mfumu Solomoni anapereka nsembe ya ng'ombe zikwi makumi awiri mphambu ziwiri, ndi nkhosa zikwi makumi awiri. Momwemo mfumu ndi anthu onse anapereka nyumba ya Mulungu.