2 Mafumu 3:5 - Buku Lopatulika Koma kunachitika, atafa Ahabu mfumu ya Mowabu anapandukana ndi mfumu ya Israele. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Koma kunachitika, atafa Ahabu mfumu ya Mowabu anapandukana ndi mfumu ya Israele. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Koma Ahabu atamwalira, mfumu ya Amowabuyo idagalukira mfumu ya ku Israele. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Koma atamwalira Ahabu, mfumu ya ku Mowabu inawukira mfumu ya ku Israeli. |
Pamenepo Elisa anamwalira, ndipo anamuika. Ndipo magulu a Amowabu analowa m'dziko poyambira chaka.