Inde akadakukopani muchoke posaukira, mulowe kuchitando kopanda chopsinja; ndipo zoikidwa pagome panu zikadakhala zonona ndithu.
2 Akorinto 6:12 - Buku Lopatulika Simupsinjika mwa ife, koma mupsinjika mumtima mwanu. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Simupsinjika mwa ife, koma mupsinjika mumtima mwanu. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Malo sakusoŵani mumtima mwathu, koma mumtima mwanu ndimo mukusoŵa malo. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ife sitikukubisirani chikondi chathu pa inu, koma inu mukubisa chikondi chanu pa ife. |
Inde akadakukopani muchoke posaukira, mulowe kuchitando kopanda chopsinja; ndipo zoikidwa pagome panu zikadakhala zonona ndithu.
Kodi adzati, Nyumba ya Yakobo iwe, Mzimu wa Yehova waperewera kodi? Izi ndi ntchito zake kodi? Mau anga samchitira zokoma kodi, iye amene ayenda choongoka?
Pakuti chipata chili chopapatiza, ndi ichepetsa njirayo yakumuka nayo kumoyo, ndimo akuchipeza chimenecho ali owerengeka.
Tipatseni malo; sitinamchitire munthu chosalungama, sitinaipse munthu, sitinachenjerere munthu.
Pakuti Mulungu ali mboni yanga, kuti ndilakalaka inu nonse m'phamphu la mwa Khristu Yesu.
Koma iye amene ali nacho chuma cha dziko lapansi, naona mbale wake ali wosowa ndi kutsekereza chifundo chake pommana iye, nanga chikondi cha Mulungu chikhala mwa iye bwanji?