Ndipo ngati mupatsa moni abale anu okhaokha, muchitanji choposa ena? Kodi angakhale anthu akunja sachita chomwecho?
2 Akorinto 13:13 - Buku Lopatulika Oyera mtima onse akupatsani moni. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Oyera mtima onse akupatsani moni. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Anthu onse a Mulungu akukupatsani moni. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Anthu onse a Mulungu akupereka moni. |
Ndipo ngati mupatsa moni abale anu okhaokha, muchitanji choposa ena? Kodi angakhale anthu akunja sachita chomwecho?
Mupatsane moni wina ndi mnzake ndi kupsompsonana kopatulika. Mipingo yonse ya Khristu ikupatsani moni.
Perekani moni kwa atsogoleri anu onse, ndi oyera mtima onse. Akupatsani moni iwo a ku Italiya.
Iye wa ku Babiloni wosankhidwa pamodzi nanu akukupatsani moni; ateronso Marko mwana wanga.