Ndipo ukatsuka chovalacho, kapena muyaro, kapena mtsendero, kapena chinthu chilichonse chopangika ndi chikopa, ngati nthenda yalekapo pa chimenecho, achitsukenso kawiri, pamenepo chili choyera.
2 Akorinto 12:8 - Buku Lopatulika Za ichi ndinapemphera Ambuye katatu kuti chichoke kwa ine. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Za ichi ndinapemphera Ambuye katatu kuti chichoke kwa ine. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Pamenepo ndidapempha Ambuye katatu kuti andichotsere chimenechi, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Katatu konse ndinapempha Ambuye kuti andichotsere. |
Ndipo ukatsuka chovalacho, kapena muyaro, kapena mtsendero, kapena chinthu chilichonse chopangika ndi chikopa, ngati nthenda yalekapo pa chimenecho, achitsukenso kawiri, pamenepo chili choyera.
Ndipo momwemonso Mzimu athandiza kufooka kwathu; pakuti chimene tizipempha monga chiyenera, sitidziwa; koma Mzimu mwini atipempherera ndi zobuula zosatheka kuneneka;
Ameneyo, m'masiku a thupi lake anapereka mapemphero ndi mapembedzero pamodzi ndi kulira kwakukulu ndi misozi kwa Iye amene anakhoza kumpulumutsa Iye muimfa, ndipo anamveka popeza anaopa Mulungu,
Kundichititsa chisoni kuti ndinaika Saulo akhale mfumu; pakuti wabwerera wosanditsata Ine, ndipo sanachite malamulo anga. Ndipo Samuele anakwiya; nalira kwa Yehova usiku wonse.