2 Akorinto 11:30 - Buku Lopatulika Ngati ndiyenera kudzitamandira, ndidzadzitamandira ndi za kufooka kwanga. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ngati ndiyenera kudzitamandira, ndidzadzitamandira ndi za kufooka kwanga. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Ngati ndiyenera kunyada, ndidzanyadira kufooka kwanga. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ngati nʼkoyenera kudzitamandira, ndidzadzitamandira pa zinthu zimene zimaonetsa kufowoka kwanga. |
Ndipo Yesu anayendayenda mu Galileya monse, analikuphunzitsa m'masunagoge mwao, nalalikira Uthenga Wabwino wa Ufumu, nachiritsa nthenda zonse ndi kudwala konse mwa anthu.
Ndiyenera kudzitamandira, kungakhale sikupindulika; koma ndidzadza kumasomphenya ndi mavumbulutso a Ambuye.
Tsopano ndikondwera nazo zowawazo chifukwa cha inu, ndipo ndikwaniritsa zoperewera za chisautso cha Khristu m'thupi langa chifukwa cha thupi lake, ndilo Mpingowo;