Baibulo la pa intaneti

Zotsatsa


Baibulo lonse Chipangano Chakale Chipangano Chatsopano




1 Samueli 20:20 - Buku Lopatulika

Ndipo ine ndidzaponya mivi itatu pambali pake, monga ngati ndilikuponya pachandamali.

Onani mutuwo

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

Ndipo ine ndidzaponya mivi itatu pambali pake, monga ngati ndilikuponya pachandamali.

Onani mutuwo

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

Ine ndidzaponya mivi itatu ku mbali ina ya muluwo, ngati ndikuchita chandamale.

Onani mutuwo

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

Ine ndidzaponya mivi itatu pambali pake, ngati ndikulasa chinthu.

Onani mutuwo



1 Samueli 20:20
3 Mawu Ofanana  

Ndipo atapita masiku atatu, utsike msanga, nufike kumene unabisala tsiku la mlandu uja, nukhale pamwala wa Ezeri.


Ndipo taona, ndidzatumiza mnyamatayo, ndi kuti, Kafune miviyo. Ndikamuuza mwanayo, kuti, Taona mivi ili chakuno; uitole nubwere, popeza pali mtendere kwa iwe, palibe kanthu, pali Yehova.


Ndipo anauza mnyamata wakeyo, Thamanga uzikatola mivi imene ndidzaponya; ndipo analikuthamanga mnyamatayu, iye anaponya muvi kuutumphitsa iye.