Ngati amuna a m'hema mwanga sanati, ndani adzapeza munthu wosakhuta nyama yomgawira Yobu?
1 Samueli 19:15 - Buku Lopatulika Ndipo Saulo anatumiza mithengayo kuti ikaone Davide, nati, Mumtengere iye pa kama wake, kuti ndidzamuphe. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo Saulo anatumiza mithengayo kuti ikaone Davide, nati, Mumtengere iye pa kama wake, kuti ndidzamuphe. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Koma Saulo adaŵatumanso anthuwo kuti akamgwire ndithu Davideyo. Adaŵauza kuti, “Mubwere naye kuno, mumnyamulire pabedi pomwepo kuti ndidzamuphe.” Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Koma Sauli anatumanso anthuwo kuti akamuone Davide, nati, “Mubwere naye kuno ali pa bedi pomwepo kuti ndidzamuphe.” |
Ngati amuna a m'hema mwanga sanati, ndani adzapeza munthu wosakhuta nyama yomgawira Yobu?
Ndipo pakulowa mithengayo, onani, pakama pali chifanizo ndi mtsamiro wa ubweya wa mbuzi kumutu kwake.