Ndiponso ndinapenyera mavuto onse ndi ntchito zonse zompindulira bwino, kuti chifukwa cha zimenezi anansi ake achitira munthu nsanje. Ichinso ndi chabe ndi kungosautsa mtima.
1 Samueli 18:29 - Buku Lopatulika Saulo nayamba kumuopa Davide kopambana; ndi Saulo anali mdani wa Davide masiku onse. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Saulo nayamba kumuopa Davide kopambana; ndi Saulo anali mdani wa Davide masiku onse. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa adamuwopabe kwambiri ndi kudana naye moyo wake wonse. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero iye anapitirirabe kumuopa Davide ndi kumadana naye moyo wake wonse. |
Ndiponso ndinapenyera mavuto onse ndi ntchito zonse zompindulira bwino, kuti chifukwa cha zimenezi anansi ake achitira munthu nsanje. Ichinso ndi chabe ndi kungosautsa mtima.
Ukhulupirira iwe kuti Mulungu ali mmodzi; uchita bwino; ziwanda zikhulupiriranso, ndipo zinthunthumira.
Ndipo Saulo anaona, nadziwa kuti Yehova ali ndi Davide; ndi kuti Mikala mwana wa Saulo anamkonda Davide.
Pomwepo mafumu a Afilisti anatuluka; ndipo nthawi zonse anatuluka iwo, Davide anali wochenjera koposa anyamata onse a Saulo, chomwecho dzina lake linatamidwa kwambiri.