Ndipo anyamata a Saulo analankhula mau awa m'makutu a Davide. Nati Davide, Kodi muchiyesera chinthu chopepuka kukhala mkamwini wa mfumu, popeza ndili munthu wosauka, ndi wopeputsidwa.
1 Samueli 18:24 - Buku Lopatulika Ndipo anyamata a Saulo anamuuza, kuti, Anatero Davide. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo anyamata a Saulo anamuuza, kuti, Anatero Davide. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Nduna za Saulo zidamuuza zonse zimene Davide adaanena. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Nduna za Sauli zinamuwuza zonse zimene anayankha Davide. |
Ndipo anyamata a Saulo analankhula mau awa m'makutu a Davide. Nati Davide, Kodi muchiyesera chinthu chopepuka kukhala mkamwini wa mfumu, popeza ndili munthu wosauka, ndi wopeputsidwa.
Nati Saulo, Mudzatero kwa Davide, kuti mfumu safuna cholowolera china, koma nsonga za makungu zana limodzi za Afilisti, kuti abwezere chilango adani a mfumu. Koma Saulo anaganizira kupha Davide ndi dzanja la Afilisti.