Yehova ndipo anati kwa iye, Mitundu iwiri ili m'mimba mwako, magulu awiri a anthu adzatuluka m'mimba mwako; gulu lina lidzapambana mphamvu ndi linzake; wamkulu adzakhala kapolo wa wamng'ono.
1 Samueli 17:14 - Buku Lopatulika Ndipo Davide anali wotsiriza; ndi akulu atatuwo anamtsata Saulo. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo Davide anali wotsiriza; ndi akulu atatuwo anamtsata Saulo. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Davide anali mzime. Ana akuluakulu atatuwo ndiwo anali ku nkhondo ndi Saulo. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Davide ndiye anali mzime. Ana aakulu atatuwo ndiwo anapita ku nkhondo ndi Sauli. |
Yehova ndipo anati kwa iye, Mitundu iwiri ili m'mimba mwako, magulu awiri a anthu adzatuluka m'mimba mwako; gulu lina lidzapambana mphamvu ndi linzake; wamkulu adzakhala kapolo wa wamng'ono.
Ndipo Samuele anati kwa Yese, Ana anu ndi omwewa kodi? Nati iye, Watsala wina, mng'ono wa onse, ndipo taonani, iye alikuweta nkhosa. Ndipo Samuele anati kwa Yese, Tumiza munthu akamtenge; pakuti ife sitidzakhala pansi kufikira iye atadza kuno.
Koma Davide akamuka kwa Saulo, nabwerera kudzadyetsa nkhosa za atate wake ku Betelehemu.