Zitapita izo, mau a Yehova anadza kwa Abramu m'masomphenya, kuti, Usaope, Abramu, Ine ndine chikopa chako ndi mphotho yako yaikulukulu.
1 Samueli 15:10 - Buku Lopatulika Pamenepo mau a Yehova anafika kwa Samuele, nati, Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Pamenepo mau a Yehova anafika kwa Samuele, nati, Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Tsono Chauta adauza Samuele kuti, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Kenaka Yehova anawuza Samueli kuti, |
Zitapita izo, mau a Yehova anadza kwa Abramu m'masomphenya, kuti, Usaope, Abramu, Ine ndine chikopa chako ndi mphotho yako yaikulukulu.
Kundichititsa chisoni kuti ndinaika Saulo akhale mfumu; pakuti wabwerera wosanditsata Ine, ndipo sanachite malamulo anga. Ndipo Samuele anakwiya; nalira kwa Yehova usiku wonse.
Koma Saulo ndi anthu anamsunga wamoyo Agagi, ndi nkhosa zokometsetsa, ndi ng'ombe, ndi zonenepa zina, ndi anaankhosa, ndi zabwino zonse sadafune kuzitha psiti; koma zonse zoipa ndi zonyansa anaziononga konsekonse.