1 Mbiri 3:3 - Buku Lopatulika wachisanu Sefatiya wa Abitala, wachisanu ndi chimodzi Itireamu wa mkazi wake Egila. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 wachisanu Sefatiya wa Abitala, wachisanu ndi chimodzi Itireamu wa mkazi wake Egila. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Mwana wake wachisanu ndi Sefatiya, mai wake anali Abitala. Mwana wake wachisanu ndi chimodzi ndi Itireamu, mai wake anali Egila. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero wachisanu anali Sefatiya, amayi ake anali Abitali; wachisanu ndi chimodzi anali Itireamu, amayi ake anali Egila. |
ndi wachisanu ndi chimodzi Itireamu wa Egila mkazi wa Davide. Awa anambadwira Davide ku Hebroni.
wachitatu Abisalomu mwana wa Maaka mwana wamkazi wa Talimai mfumu ya Gesuri, wachinai Adoniya mwana wa Hagiti,
Anambadwira asanu ndi mmodzi mu Hebroni; ndi pomwepo anakhala mfumu zaka zisanu ndi ziwiri, ndi miyezi isanu ndi iwiri; ndi mu Yerusalemu anakhala mfumu zaka makumi atatu mphambu zitatu.