1 Mbiri 2:9 - Buku Lopatulika Ndi ana a Hezironi anambadwirawo: Yerameele, ndi Ramu, ndi Kalebe. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndi ana a Hezironi anambadwirawo: Yerameele, ndi Ramu, ndi Kalebe. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Ana amene adabereka Hezironi naŵa: Yerameele, Ramu ndi Kelebe. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ana amene anabadwa kwa Hezironi anali: Yerahimeeli, Ramu ndi Kelubai. |
Ndipo atafa Hezironi mu Kalebe-Efurata, Abiya mkazi wa Hezironi anambalira Asiriya atate wa Tekowa.
Ndi ana a Yerameele mwana woyamba wa Hezironi ndiwo: woyamba Ramu, ndi Buna, ndi Oreni, ndi Ozemu, ndi Ahiya.
Ndi ana a Kalebe mbale wa Yerameele ndiwo Mesa mwana wake woyamba, ndiye atate wa Zifi; ndi ana a Maresa atate wa Hebroni.
ndi Yuda anabala Perezi ndi Zera mwa Tamara; ndi Perezi anabala Hezironi; ndi Hezironi anabala Ramu;
Ndipo iye anadza kudziko lonse la m'mbali mwa Yordani, nalalikira ubatizo wa kulapa mtima kuloza ku chikhululukiro cha machimo;
Ndipo Akisi anati, Waponyana nkhondo ndi yani lero? Nati Davide, Ndi a kumwera kwa Ayuda, ndi a kumwera kwa Ayerameele, ndi a kumwera kwa Akeni.