1 Mbiri 1:3 - Buku Lopatulika Enoki, Metusela, Lameki, Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Enoki, Metusela, Lameki, Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Yaredi adabereka Enoki, Enoki adabereka Metusela, Metusela adabereka Lameki, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Enoki, Metusela, Lameki, Nowa. |
Ndi chikhulupiriro Enoki anatengedwa kuti angaone imfa; ndipo sanapezeke, popeza Mulungu adamtenga: pakuti asanamtenge, anachitidwa umboni kuti anakondweretsa Mulungu;
Ndipo kwa iwo, Enoki, wachisanu ndi chiwiri kuyambira kwa Adamu, ananenera kuti, Taona, wadza Ambuye ndi oyera ake zikwi makumi,