Ndipo ananyamuka nthawi yomweyo nabwera ku Yerusalemu, napeza khumi ndi mmodziwo, ndi iwo anali nao atasonkhana pamodzi,
1 Akorinto 15:7 - Buku Lopatulika pomwepo anaonekera kwa Yakobo; pamenepo kwa atumwi onse; Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 pomwepo anaonekera kwa Yakobo; pamenepo kwa atumwi onse; Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Ndipo adaonekera Yakobe, kenaka atumwi onse. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Kenaka anaonekeranso kwa Yakobo, kenaka kwa atumwi onse. |
Ndipo ananyamuka nthawi yomweyo nabwera ku Yerusalemu, napeza khumi ndi mmodziwo, ndi iwo anali nao atasonkhana pamodzi,
Ndipo pakulankhula izi iwowa, Iye anaimirira pakati pao; nanena nao, Mtendere ukhale nanu.
Koma m'mene adawatambasulira dzanja akhale chete, anawafotokozera umo adamtulutsira Ambuye m'ndende. Ndipo anati, Muwauze Yakobo ndi abale izi. Ndipo anatuluka napita kwina.