1 Akorinto 12:5 - Buku Lopatulika Ndipo pali mautumiki osiyana, koma Ambuye yemweyo. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo pali mautumiki osiyana, koma Ambuye yemweyo. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Pali njira zosiyanasiyana zotumikira, koma Ambuye amene timaŵatumikira ndi amodzimodzi. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Pali mautumiki osiyanasiyana koma Ambuye yemweyo. |
Mau amene anatumiza kwa ana a Israele, akulalikira Uthenga Wabwino wa mtendere mwa Yesu Khristu (ndiye Ambuye wa onse)
koma kwa ife kuli Mulungu mmodzi, Atate amene zinthu zonse zichokera kwa Iye, ndi ife kufikira kwa Iye; ndi Ambuye mmodzi Yesu Khristu, amene zinthu zonse zili mwa Iye, ndi ife mwa Iye.