1 Akorinto 11:8 - Buku Lopatulika Pakuti mwamuna sakhala wa kwa mkazi; koma mkazi wa kwa mwamuna; Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Pakuti mwamuna sakhala wa kwa mkazi; koma mkazi wa kwa mwamuna; Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Pajatu mwamuna sadapangidwe kuchokera kwa mkazi, koma mkazi ndiye adapangidwa kuchokera kwa mwamuna. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Pakuti mwamuna sachokera kwa mkazi, koma mkazi kwa mwamuna. |