1 Akorinto 11:13 - Buku Lopatulika Lingirirani mwa inu nokha: Kodi nkuyenera kuti apemphere kwa Mulungu, wosafunda mutu? Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Lingirirani mwa inu nokha: Kodi nkuyenera kuti apemphere kwa Mulungu, wosafunda mutu? Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Weruzani nokha ngati nkoyenera kuti mkazi azipembedza Mulungu osavala kanthu kumutu. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Dziweruzeni. Kodi nʼchabwino kuti mkazi apemphere kwa Mulungu wopanda chophimba kumutu? |
Akazi akhale chete mu Mipingo. Pakuti sikuloledwa kwa iwo kulankhula. Koma akhale omvera, monganso chilamulo chinena.