Ndipo Israele anaiona ntchito yaikulu imene Yehova anachitira Aejipito, ndipo anthuwo anaopa Yehova; nakhulupirira Yehova ndi mtumiki wake Mose.
1 Akorinto 10:2 - Buku Lopatulika nabatizidwa onse kwa Mose, mumtambo, ndi m'nyanja, Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 nabatizidwa onse kwa Mose, mumtambo, ndi m'nyanja, Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Motero mumtambomo ndi m'nyanjamo onsewo adachita ngati kubatizidwa ndi kukhala amodzi ndi Mose. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ndipo onse anabatizidwa mwa Mose mu mtambo ndi mʼnyanja. |
Ndipo Israele anaiona ntchito yaikulu imene Yehova anachitira Aejipito, ndipo anthuwo anaopa Yehova; nakhulupirira Yehova ndi mtumiki wake Mose.
Kapena kodi simudziwa kuti ife tonse amene tinabatizidwa mwa Khristu Yesu; tinabatizidwa mu imfa yake?