Chifukwa chake mukani, phunzitsani anthu a mitundu yonse, ndi kuwabatiza iwo m'dzina la Atate, ndi la Mwana, ndi la Mzimu Woyera:
1 Akorinto 1:15 - Buku Lopatulika kuti anganene mmodzi kuti mwabatizidwa m'dzina langa. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 kuti anganene mmodzi kuti mwabatizidwa m'dzina langa. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Motero palibe amene anganene kuti adabatizidwa m'dzina langa. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero mwakuti palibe amene anganene kuti anabatizidwa mʼdzina langa. |
Chifukwa chake mukani, phunzitsani anthu a mitundu yonse, ndi kuwabatiza iwo m'dzina la Atate, ndi la Mwana, ndi la Mzimu Woyera:
Iye wolankhula zochokera kwa iye yekha afuna ulemu wa mwini yekha. Iye wakufuna ulemu wa Iye amene anamtuma, yemweyu ali woona, ndipo mwa Iye mulibe chosalungama.
Koma ndinabatizanso a pa banja la Stefanasi; za ena, sindidziwa ngati ndinabatiza wina yense.
Pakuti ndichita nsanje pa inu ndi nsanje ya Mulungu; pakuti ndinakupalitsani ubwenzi mwamuna mmodzi, kuti ndikalangize inu ngati namwali woyera mtima kwa Khristu.