Buku Lopatulika Buku Lopatulika Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
Nahumu Genesis Eksodo Levitiko Numeri Deuteronomo Yoswa Oweruza Rute 1 Samueli 2 Samueli 1 Mafumu 2 Mafumu 1 Mbiri 2 Mbiri Ezara Nehemiya Estere Yobu Masalimo Miyambo Mlaliki Nyimbo ya Solomoni Yesaya Yeremiya Maliro Ezekieli Danieli Hoseya Yoweli Amosi Obadiya Yona Mika Nahumu Habakuku Zefaniya Hagai Zekariya Malaki Mateyu Marko Luka Yohane Machitidwe a Atumwi Aroma 1 Akorinto 2 Akorinto Agalatiya Aefeso Afilipi Akolose 1 Atesalonika 2 Atesalonika 1 Timoteyo 2 Timoteyo Tito Filemoni Ahebri Yakobo 1 Petro 2 Petro 1 Yohane 2 Yohane 3 Yohane Yuda Chivumbulutso
Mutu INTRO1 Mutu 1 Mutu 2 Mutu 3
Nahumu INTRO1 - Buku Lopatulika Buku Lopatulika Nahumu INTRO1 1
Mau Oyamba
Bukuli ndi ndakatulo yokondwerera kupasuka kwa Ninive, mzinda waukulu wa Aasiriya amene ankazunza Aisraele kuyambira kale. Kupasuka kwa mzindawo kuwoneka ngati chilango cha Mulungu chogwera anthu onyada ndi ankhanza.
Za mkatimu
Chauta aimba Ninive mlandu 1.1-15
Kupasuka kwa mzindawo 2.1—3.19