Baibulo la pa intaneti

Zotsatsa

Baibulo lonse Chipangano Chakale Chipangano Chatsopano


Hagai INTRO1 - Buku Lopatulika Buku Lopatulika
Hagai INTRO1

1

Mau Oyamba
Mneneriyu adalalika mau ake chaka cha 520 BC., Ayuda ena atabwerera ku Yerusalemu kuchokera ku ukapolo. Anthuwo anali atabwerera ku ukapolo namakhala ku Yerusalemu kwa zaka zingapo, koma Kachisi anali bwinja lenileni. Atsogoleri anapereka uthenga kwa anthu kuti amangenso Kachisi, ndipo Ambuye akulonjeza kuti m'tsogolo anthu ake adzakhala pabwino ndi pa mtendere.
Za mkatimu
Yehova awalamula kuti amangenso Nyumba yake 1.1-15
Mau ena owalimbitsa mtima Ayudawo 2.1-23

Bible Society of Malawi

Bible Society of Malawi