3 Lizani wunda pakukhala kwamwezi, pakukhuma kwamwezi, pantsiku yathu yafeshita.
Lekani adumbize dzina lake nakubvina! Achimuyimbila, achiliza chikhwechele nachipendani!
Tendani Chawuta nachipendani! Mupembezeni nagitale lina mawaya khumi!
Nawunda, nakulila kwanyanga, chitani chiwowo chakusekelela pamaso pa Mambo Chawuta!