8 Lekani atonge kuchoka kunyanja kafika kunyanja! Kuchoka kukamadzi kafika kumpelela dziko!
Ndikumbile, ndikupase mishowo yawanthu kuti ikhale nthaka yako, nadziko kufika kumapeto kwalene.
mithayi yeyene ichitambalala kufika kunyanja, namizi yayene kufika kukamadzi kakulu.
Nin'zayikha janja lake panyanja, janja lake ladidi patukamadzi.
M'badwe wake un'zakhala kufika lini nalini, mpando wake un'zakhala ninga dzuwa pamaso pangu.