1 Imwe Mulungu pasani mambo kulinganiza kwanu! Mwana wamambo chilungamo chanu!
Kunja kwakuti Chawuta ndiye wamanga nyumba, aniyimangawo am'manga papezi. Kunja kwakuti Chawuta ndiye wakhaliliza guta, akhalilizi an'khaliliza papezi.