36 Wana waalanda wake an'zayachita nthaka yawo, awo anfuna dzina lake an'zakhala m'mwemo.
Wana waalanda wanu an'zakhala mwakuchinjilizika, mibadwe yawo in'zakhazikisiwa pamaso panu.
Wakulungama an'zatola dziko, an'zakhalamo kufika lini nalini.
“Pakuti wamamatila payine, nin'zamupulumusa, nin'zamuchinjiliza, thangwe lakuti an'dziwa dzina langu.