24 Thululani ukali wanu kwayiwo! Nkwiyo wanu uwafikile!
Thululilani ukali wanu kwawanthu wakunja ansaya kukudziwani, nakuwumambo uzinji unsaya kuchemela dzina lanu!