6 Dziko lidabulisa bzakukolola, Mulungu, Mulungu wathu an'zatidalisa!
Nin'zachita chibvano changu pakati payine nayiwe, nakum'badwe un'zabwela pambuyo pako, pakuti nichibvano chin'khala kufika lini nalini. Ine nin'zakhala Mulungu wako mpaka kum'badwe wako wentse um'bwela.
pakuti uyu ni Mulungu wathu, kufika lini nalini, an'zatitsogolela kufika kufa.