13 Leka ntima wako uwone kuchinjilizika, pitani mumbuto zake zakubzichinjiliza, kuti muzawuzembo m'badwe um'bwela,
Nkhalo ngayikhale nkati mwamipanda yanu, pomwe n'delekho ukhale nkati mwamadala yanu!
Kufikila ndakalamba, kufikila ndachena nsolo, imwe Mulungu lekani kundisiya! Kufikila ndalalikila bzamphamvu zanu kum'badwe unango, mphamvu zanu, kwawentse am'bwela.