7 Nakutenepo ine ndidati, “Yinde ndabwela, mubhuku lamitemo mudanembewa nabzangu.
Nin'zayikha chizondo pakati payiwe nankazi, pakati pawana wake nawana wako. An'zaphwanya nsolo wako, iwe un'zaluma chithatha chake.”
Nin'zatambila lini ng'ombe imuna kuchoka nyumba mwako, panango tonde kuchokela m'mathanga yanu.
Chitilani bzabwino Ziyoni, mukukoma ntima kwanu, mangani pomwe mpanda waku Jerusalema.