3 Mudumbizeni nakulila kwawunda! Mudumbizeni nantolilo nachipendani!
Lamuka, iwe banjo nachipendani! Nin'zalamusa madandakucha!
Lekani adumbize dzina lake nakubvina! Achimuyimbila, achiliza chikhwechele nachipendani!
Tendani Chawuta nachipendani! Mupembezeni nagitale lina mawaya khumi!
ndichiyimba nantolilo nabhanjo, nakulila kwachipendani.