3 uyo ansaya kulewa magunkha. Ansaya kuchitila mwanzake chakuyipa, ansaya kunyoza dzina lawaan'khala naye.