2 Pamiti yamupopula, tidamanika bzipendani bzathu pamwepo.
Tendani Chawuta nachipendani! Mupembezeni nagitale lina mawaya khumi!
Tsamulani nyimbo, lizani chikhwechele! Lizani chipendani nabhanjo!