3 Anilekelela lini, nzayo zako zichitelela, aniwodzila lini, uyo ankuchengeta.
Kunja kwakuti Chawuta ndiye wamanga nyumba, aniyimangawo am'manga papezi. Kunja kwakuti Chawuta ndiye wakhaliliza guta, akhalilizi an'khaliliza papezi.
Chawuta animuchengeta achimulalamisa, achikhala ali bwino padziko, aniwalekelela lini kwaazondi wawo.
Koma imwe Mulungu mun'zathusila wakuyipa wentse m'manda, wanthu wagazi nawachinyengo, an'zalalama ne kati-nakati yantsiku zawo. Koma ine nin'zathemba nayimwe.
Adatifuwa pakati pawanthu, alibe kuleka minyendo yathu ichipsedemuka.
An'zakutakula m'manja mwawo, kuti nzayo yako ileke kukhukhumudwa namwala.