12 Ninga kutalamukana kwamabveladzuwa namadokelo, ndiko kutalamusa bzakuyipa bzathu kwaadachita.
Kuyambila pakuchoka kwadzuwa, mpaka kudoka kwalene, dzina la Chawuta ngalidumbiziwe!
Wam'phamvu, Mulungu Chawuta, anilewa achichemela dziko lapantsi, kuyambila kumabveladzuwa mpaka kumadokelo.