Kuyamba 17:7 - Bhukhu la Kuyamba7 Nin'zachita chibvano changu pakati payine nayiwe, nakum'badwe un'zabwela pambuyo pako, pakuti nichibvano chin'khala kufika lini nalini. Ine nin'zakhala Mulungu wako mpaka kum'badwe wako wentse um'bwela. အခန်းကိုကြည့်ပါ။ |