31 Iyi ndiyo nthaka yam'badwe wa Asheri kuteyeza mabanja yawo, maguta yamweya namiyi yawo.
“Chakudya cha Asheri chin'zakhala namafuta, an'zakolola chakudya chawumambo.”
na Uma na Afeki na Rehobhi, maguta yentse yakhali makumi mawili namawili namiyi yayene.
Kuwombeza kwachitanthatu kudafikila m'badwe wa Nafitali kuteyeza mabanja yawo.